Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Ezara 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakupemphera Ezara tsono, ndi kuulula ndi kulira misozi, ndi kudzigwetsa pansi pakhomo pa nyumba ya Mulungu, udamsonkhanira mwa Israyeli msonkhano waukuru ndithu wa amuna, ndi akazi, ndi ana; popeza anthu analira kulira, kwakukuru.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:1 nkhani