Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiwo masiku amene Ayuda anapumula pa adani ao; ndi mwezi wacisoni unawasandulikira wakukondwera, ndi wamaliro ukhale tsiku lokoma, awayese masiku amadyerero ndi akukondwera, akutumizirana magawo, ndi akupatsa zaufulu kwa osauka.

Werengani mutu wathunthu Estere 9

Onani Estere 9:22 nkhani