Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo mfumu Ahaswero anampatsa mkazi wamkuru Estere nyumba ya Hamani mdani wa Ayuda, Nafika Moredekai pamaso pa mfumu; pakuti Estere adamuuza za cibale cace.

Werengani mutu wathunthu Estere 8

Onani Estere 8:1 nkhani