Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nibwera mfumu ku munda wa maluwa wa kucinyumba kulowanso m'nyumba munali madyerero a vinyo, napeza Hamani atagwa pa kama wokhalapo Estere. Niti mfumu, Kodi aumiriza mkazi wamkuru pamaso panga m'nyumba? Poturuka mau pakamwa pa mfumu anamphimba Hamani nkhope.

Werengani mutu wathunthu Estere 7

Onani Estere 7:8 nkhani