Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 7:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pakuti tagulitsidwa; ine ndi anthu amtundu wanga, kuti ationonge, atiphe, natipulule, Koma tikadagulitsidwa tikhale akapolo ndi adzakazi, ndikadakhala cete; cinkana wosautsa sakadakhoza kubwezera kusowa kwa mfumu.

Werengani mutu wathunthu Estere 7

Onani Estere 7:4 nkhani