Napeza mudalembedwa kuti Moredekai adaulula za Bigitana ndi Teresi, awiri a adindo a mfumu osunga pakhomo, amene adayesa kumthira manja mfumu Ahaswero.