Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hamani anafotokozera Zeresi mkazi wace, ndi mabwenzi ace onse, zonse zidamgwera, Nanena naye anzeru ace, ndi Zeresi mkazi wace, Moredekai amene wayamba kutsika pamaso pace, akakhala wa mbumba ya Ayuda, sudzamlaka; koma udzagwada pamaso pace.

Werengani mutu wathunthu Estere 6

Onani Estere 6:13 nkhani