Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 6:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hamani anatenga cobvala ndi kavalo, nabveka Moredekai, namuyendetsa pa kavalo m'khwalala la m'mudzi, napfuula pamaso pace, Azitero naye munthu amene mfumu ikondwera kumcitira ulemu.

Werengani mutu wathunthu Estere 6

Onani Estere 6:11 nkhani