Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 6:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu inati kwa Hamani, Fulumira, tenga cobvala ndi kavalo monga umo wanenera, nucitire cotero Moredakai Myudayo, wokhala pa cipata ca mfumu; kasasowepo kanthu ka zonse wazinena.

Werengani mutu wathunthu Estere 6

Onani Estere 6:10 nkhani