Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 10:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Moredekai Myuda anatsatana naye mfumu Ahaswero, nakhala wamkuru mwa Ayuda, nabvomerezeka mwa unyinji wa abale ace wakufunira a mtundu wace zokoma, ndi wakunena za mtendere kwa mbeu yace yonse.

Werengani mutu wathunthu Estere 10

Onani Estere 10:3 nkhani