Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

caka cacitatu ca ufumu wace, anakonzera madyerero akalonga ace onse, ndi omtumikira; amphamvu a Perisiya ndi Mediya, omveka ndi akalonga a maikowo anakhala pamaso pace,

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:3 nkhani