Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 9:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Farao anaona kuti mvula ndi matalala ndi mabingu zidaleka anaonjezanso kucimwa, naumitsa mtima wace, iye ndi anyamata ace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 9

Onani Eksodo 9:34 nkhani