Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 8:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Uuke ulawire mamawa, nuime pamaso pa Farao; taona, aturuka kumka kumadzi; nunene naye, Atero Yehova, Lola anthu anga amuke, anditumikire.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 8

Onani Eksodo 8:20 nkhani