Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 7:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ndi Aroni anacita monga momwe Yehova adawalamulira; nasamula ndodo, napanda madzi ali m'nyanjamo pamaso pa Farao, ndi pamaso pa anyamata ace; ndipo madzi onse a m'nyanjamo anasanduka mwazi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7

Onani Eksodo 7:20 nkhani