Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 7:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova anati kwa Mose, Nena ndi Aroni, Tenga ndodo yako, nutambasule dzanja lako pa madzi a m'Aigupto, pa nyanja yao, pa ngalande zao, ndi pa matamanda ao, ndi pa matawale ao onse amadzi, kuti asanduke mwazi; mukhale mwazi m'dziko lonse la Aigupto, m'zotengera zamtengo, ndi zamwala.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7

Onani Eksodo 7:19 nkhani