Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose ananena comweco ndi ana a Israyeli; koma sanamvera Mose cifukwa ca kuwawa mtima, ndi ukapolo wolemera.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:9 nkhani