Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzakulowetsani m'dziko limene ndinakweza dzanja langa kunena za ilo, kuti ndilipereke kwa Abrahamu, kwa Isake ndi kwa Yakobo; ndipo ndidzakupatsani ilo likhale lanulanu; Ine ndine Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:8 nkhani