Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace nena kwa ana a Israyeli, Ine ndine Yehova, ndipo ndidzakuturutsani pansi pa akatundu a Aaigupto, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wanu; ndipo ndidzakuombolani ndi dzanja lotambasuka, ndi maweruzo akuru;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:6 nkhani