Popeza kuyambira kuja ndinafika kwa Farao kulankhula m'dzina lanu, anawacitira coipa anthuwa; ndipo simunalanditsa anthu anu konse.