Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa Yehova, Mverani, Ambuye, ine ndine munthu wosowa ponena, kapena dzulo, kapena kale, kapena cilankhulire Inu ndi kapolo wanu, pakuti ndine wa m'kamwa molemera, ndi wa lilime lolemera.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:10 nkhani