Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamanga capacifuwa pa mphete zace ndi mphete za efodi ndi mkuzi wamadzi, kuti cikhale pa mpango wa efodi, ndi kuti capacifuwa cisamasuke paefodi; monga Yehova anamuuza Mose.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:21 nkhani