Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga mphete ziwiri zagolidi, naziika pa zapamapewa ziwiri za efodi pansi pace, pa mbali yace ya kutsogolo, pafupi pa msoko wace, pamwamba pa mpango wa efodi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:20 nkhani