Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 37:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga guwa la nsembe lofukizapo la mtengo wasitimu; utali wace mkono, ndi kupingasa kwace mkono, lampwamphwa; ndimsinkhu wace mikono iwiri; nyanga zace zinaturuka m'mwemo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 37

Onani Eksodo 37:25 nkhani