Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 37:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Bezaleli anapanga likasa la mtengo wasitimu; utali wace mikono iwiri ndi hafu, ndi kupingasa kwace mkono ndi hafu, ndi msinkhu wace mkono ndi hafu;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 37

Onani Eksodo 37:1 nkhani