Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 36:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Utali wace wa nsaru yophimba imodzi ndiwo mikono makumi awiri kudza isanu ndi itatu, ndi kupingasa kwace kwa nsaru imodzi mikono inai; nsaru zonse zinafanana muyeso wao.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:9 nkhani