Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 36:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse a mtima waluso mwa iwo akucita nchitoyi anapanga kacisi ndi nsaru zophimba khumi; anaziomba ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi lamadzi; ndi lofiira, ndi lofiira, ndi akerubi, nchito ya mmisiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:8 nkhani