Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 36:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analandira kwa Mose copereka conse, cimene ana a Israyeli adabwera naco cikhale ca macitidwe a nchito ya malo opatulika, aipange naco. Koma anaonjeza kubwera nazo kwa iye zopereka zofuna mwini, m'mawa ndi m'mawa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:3 nkhani