Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 36:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose adaitana Bezaleli ndi Aholiabu, ndi anthu onse aluso, amene Yehova adaika luso m'mtima mwao, onse ofulumidwa mtima ayandikize kunchito kuicita.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:2 nkhani