Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 35:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amenewo anawadzaza ndi luso lamtima, lakucita nchito ziri zonse, ya kuzokota miyala, ndi ya mmisiri waluso, ndi ya wopikula ndi lamadzi ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa, ndi ya muomba, ya iwo akucita nchito iri yonse, ndi ya iwo olingirira nchito yaluso.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 35

Onani Eksodo 35:35 nkhani