Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 35:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza amuna ndi akazi, onse akufuna mtima eni ace, nabwera nazo mphete za mphuno, mphete za m'makutu, ndi mphete zosindikizira, ndi zidzingwiri, zonsezi zokometsera zagolidi; inde yense wakupereka kwa Yehova copereka cagolidi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 35

Onani Eksodo 35:22 nkhani