Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 33:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye anati, Ndidzapititsa ukoma wanga wonse pamaso pako, ndipo ndidzachula dzina la Yehova pamaso pako; ndipo ndidzacitira ufulu amene ndidzamcitira ufulu; ndi kucitira cifundo amene ndidzamcitira cifundo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 33

Onani Eksodo 33:19 nkhani