Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 33:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anati kwa Yehova, Taonani, Inu munena ndi ine, Kwera nao anthu awa; koma simunandidziwitsa amene mudzamtuma amuke nane. Koma munati, Ndikudziwa dzina lako, wapezanso ufulu pamaso panga,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 33

Onani Eksodo 33:12 nkhani