Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma mkazi yense adzafunse mnzace, ndi mlendo wokhala m'nyumba mwace, ampatse zokometsera zasiliva, ndi zokometsera zagolidi, ndi zobvala; ndipo mudzabveke nazo ana anu amuna ndi akazi; ndipo mudzafunkhe za Aaigupto.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:22 nkhani