Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzapatsa anthu awa ufulu pamaso pa anthu a Aigupto; ndipo kudzakhala, pamene muturuka simudzaturuka opanda kanthu;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:21 nkhani