Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wa Molungu anamuonekera m'cirangali camoto coturuka m'kati mwa citsamba; ndipo anapenya, ndipo taonani, citsamba cirikuyaka moto, koma cosanyeka citsambaco.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:2 nkhani