Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mose analikuweta gulu la Yetero mpongozi wace, wansembe wa ku Midyani; natsogolera gululo m'tsogolo mwa cipululu, nafika ku phiri la Mulungu, ku Horebe.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:1 nkhani