Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muka, nukasonkhanitse akuru a Israyeli, nunene nao, Yehova, Mulungu wa makolo anu anandionekera ine, Mulungu wa Abrahamu, Isake ndi Yakobo, ndi kuti; Ndakuzondani ndithu, ndi kuona comwe akucitirani m'Aigupto;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:16 nkhani