Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mulungu ananenanso kwa Mose, Ukatero ndi ana a Israyeli, Yehova, Molungu wa makolo anu, Molungu wa Abrahamu, Mulungu wa Isake, ndi Molungu wa Yakobo anandituma kwa inu; ili nw dzina langa nthawi yosatha, ici ndi cikumbukiro canga m'mibadwo mibadwo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:15 nkhani