Ikhale nsembe yopsereza yosalekeza ya mwa mibadwo yanu, pa khomo la cihema cokomanako, pamaso pa Yehova, kumene ndidzakomana nanu, kulankhula nawe komweko.