Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 29:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ikatsalako nyama yodzaza manja, kapena mkate kufikira m'mawa, pamenepo utenthe zotsalazo ndi moto; asazidye popeza ncopatulika ici.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 29

Onani Eksodo 29:34 nkhani