Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cizikhala pamphumi pace pa Aroni, ndipo Aroni azinyamula mphulupulu ya zopatulidwa, zimene ana a Israyeli azipatulira, ndi zopereka zao zonse zopatulira; ndipo cizikhala pamphumi pace kosalekeza, kuti alandiridwe pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:38 nkhani