Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 28:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uike Urimu ndi Tumimu mwa capacifuwa ca ciweruzo; ndipo zikhale pa mtima wa Aroni, pakulowa iye pamaso pa Yehova; ndipo Aroni azinyamula ciweruzo ca ana a Israyeli pamtima pace pamaso pa Yehova kosalekeza.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 28

Onani Eksodo 28:30 nkhani