Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 27:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Utali wace wa bwalolo ukhale wa mikono zana limodzi, ndi kupingasa kwace makumi asanu monsemo, ndi msinkhu wace wa mpanda mikono isanu; ukhale wabafuta wa thonje losansitsa; ndi makamwa a nsicizo akhale amkuwa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 27

Onani Eksodo 27:18 nkhani