Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 26:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzipangira nsaru yotsekerayo nsanamira zisanu za mtengo wasitimu, ndi kuzikuta ndi golidi; zokowera zao zikhale zagolidi; nuziyengera makamwa asanu amkuwa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:37 nkhani