Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 26:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uzipanga zokowera makumi asanu zamkuwa, ndi kukowetsa zokowerazo m'magangomo, ndi kumanga pamodzi hemalo likhale limodzi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 26

Onani Eksodo 26:11 nkhani