Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 24:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose analembera mau onse a Yehova, nalawira kuuka mamawa, namanga guwa la nsembe patsinde pa phiri, ndi zoimiritsa khumi ndi ziwiri, kwa mafuko khumi ndi awiri a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 24

Onani Eksodo 24:4 nkhani