Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 24:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mose anadza nafotokozera anthu mau onse a Yehova, ndi masveruzo onse; ndipo anthu onse anabvomera pamodzi, nati, Mau onse walankhula Yehova tidzacita.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 24

Onani Eksodo 24:3 nkhani