Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 23:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uzikhala kutali ndi mlandu wonama; ndipo usapha munthu wosacimwa ndi wolungama; pakuti sindidzayesa wolungama munthu woipa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 23

Onani Eksodo 23:7 nkhani