Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 21:35-36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

35. Ng'ombe ya mwini ikapweteka ng'ombe ya mnzace, nifa, azigulitsa ng'ombe yamoyoyo, nagawe ndalama zace; naigawe, ndi yakufa yomweyo.

36. Kapena kudadziwika kuti ng'ombeyo ikatunga masiku adapitawo, koma osaisunga mwiniyo, azilipa ndithu, ng'ombe kulipa ng'ombe, koma yakufayo ndi yace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21