Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 21:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ng'ombe ya mwini ikapweteka ng'ombe ya mnzace, nifa, azigulitsa ng'ombe yamoyoyo, nagawe ndalama zace; naigawe, ndi yakufa yomweyo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 21

Onani Eksodo 21:35 nkhani